Zekariya 9:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova Mulungu wao adzawapulumutsa tsiku ilo, ngati zoweta za anthu ace; pakuti adzakhala ngati miyala ya m'korona yakunyezimira pa dziko lace.

Zekariya 9

Zekariya 9:11-17