Zekariya 9:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova wa makamu adzawacinjiriza; ndipo adzadza, nadzapondereza miyala yoponyera; ndipo adzamva, nadzacita phokoso ngati avinyo; ndipo adzadzazidwa ngati mbale, ngati ngondya za guwa la nsembe.

Zekariya 9

Zekariya 9:13-17