Zekariya 9:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ukoma wace ndi waukuru ndithu, ndi kukongola kwace nkwa kukuru ndithu! tirigu adzakometsera anyamata, ndi vinyo watsopano anamwali.

Zekariya 9

Zekariya 9:10-17