Zekariya 13:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzacitika, akaneneranso wina, atate wace ndi mai wace ombala adzanena naye, Sudzakhala ndi moyo, pakuti unena bodza m'dzina la Yehova; ndipo atate wace ndi mai wace ombala adzamgwaza ponenera iye.

Zekariya 13

Zekariya 13:2-4