Zekariya 13:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzacitika tsiku lomwelo, ati Yehova wa makamu, ndidzaononga maina a mafano m'dziko; ndipo sadzakumbukikanso; ndipo ndidzacotsa m'dziko aneneri ndi mzimu wacidetso.

Zekariya 13

Zekariya 13:1-5