Zekariya 13:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzacitika tsiku lomwelo kuti aneneri adzacita manyazi yense ndi masomphenya ace, ponenera iye; ndipo sadzabvala copfunda caubweya kunyenga naco;

Zekariya 13

Zekariya 13:1-9