Yoswa 7:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa anatuma amuna kucokera ku Yeriko apite ku Ai, ndiwo pafupi pa Beti-aveni, kum'mawa kwa Beteli; nanena nao, Kwerani ndi kukazonda dziko. Nakwera amunawo, nazonda Ai.

Yoswa 7

Yoswa 7:1-3