Yoswa 7:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ana a Israyeli analakwa ndi coperekedwaco; popeza Akani mwana wa Karimi, mwana wa Zabidi, mwana wa Zera, wa pfuko la Yuda, anatapa coperekedwaco; ndi mkwiyo wa Yehova unayakira ana a Israyeli.

Yoswa 7

Yoswa 7:1-3