Yoswa 7:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anabwera kwa Yoswa, nati kwa iye, Asakwere anthu onse; koma akwere amuna ngati zikwi ziwiri kapena zitatu kukantha Ai; musalemetsa anthu onse kumkako, pakuti a komweko ndi owerengeka;

Yoswa 7

Yoswa 7:1-6