Yoswa 20:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iyi ndi midzi yoikidwira ana onse a Israyeli, ndi mlendo wakukhala pakati pao, kuti athawireko ali yense wakupha munthu, ndi kuti asafe ndi dzanja la wolipsa mwazi, asanaime pamaso pa msonkhano.

Yoswa 20

Yoswa 20:6-9