Yoswa 20:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsidya lija la Yordano kum'mawa kwa Yeriko, anaika Bezeri m'cipululu, kucidikha, wa pfuko la Rubeni, ndi Ramoti m'Gileadi wa ofuko la Gadi, ndi Golani m'Basana wa pfuko la Manase.

Yoswa 20

Yoswa 20:2-9