Yoswa 21:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo akuru a nyumba za atate a Alevi anayandikira kwa Eleazare wansembe, ndi kwa Yoswa mwana wa Nuni, ndi kwa akuru a nyumba za atate a mapfuko a ana a Israyeli;

Yoswa 21

Yoswa 21:1-2