Yohane 4:46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Yesu anadzanso ku Kana wa m'Galileya, kumene anasandutsa madzi vinyo. Ndipo kunalimkulu wina wa mfumu, mwana wace anadwala m'Kapernao.

Yohane 4

Yohane 4:36-49