Yohane 4:47 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iyeyu, pamene anamva kuti Yesu wacokera ku Yudeya nafika ku Galileya, ananka kwa iye, nampempha kuti atsike kukaciritsa mwana wace; pakuti anali pafupi imfa.

Yohane 4

Yohane 4:39-49