Yohane 4:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace pamene anadza ku Galileya, Agalileva anamlandira iye, atakaona zonse zimene anazicita m'Yerusalemu paphwando; pakuti iwonso ananka kuphwando.

Yohane 4

Yohane 4:38-47