Yohane 18:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma Petro anaima kukhomo kunja, Cifukwa cace wophunzira winayo amene anadziwika kwa mkulu wa ansembe, anaturuka nalankhula ndi wapakhomo, nalowetsa Petro.

Yohane 18

Yohane 18:6-26