Yohane 18:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Simoni Petro ndi wophunzira wina anatsata Yesu. Koma wophunzira ameneyo anali wodziwika kwa mkulu wa ansembe, nalowa pamodzi ndi Yesu, m'bwalo la mkulu wa ansembe;

Yohane 18

Yohane 18:14-21