Yohane 18:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo namwali wapakhomoyo ananena kwa Petro, Kodi suli iwenso wa akuphunzira a munthu uyu? Iyeyu ananena, Sindine.

Yohane 18

Yohane 18:15-18