Yohane 12:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ngati wina anditumikira Ine, anditsate; ndipo kumene kuli Ine, komwekonso kudzakhala mtumiki wanga, Ngati wina anditumikira Ine, Atate adzamcitira ulemu iyeyu,

Yohane 12

Yohane 12:17-29