Yohane 12:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Moyo wanga wabvutika tsopano; ndipo ndidzanena ciani? Atate, ndipulumutseni Ine ku nthawi iyi. Koma cifukwa ca ici ndinadzera nthawi iyi.

Yohane 12

Yohane 12:23-28