Yohane 12:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iye wokonda moyo wace adzautaya; ndipo wodana ndi moyo wace m'dziko lino lapansi adzausungira ku moyo wosatha.

Yohane 12

Yohane 12:23-32