Yesaya 6:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Caka cimene mfumu Uziya anafa, ndinaona Ambuye atakhala pa mpando wacifumu wautari, ndi wotukulidwa, ndi zobvala zace zinadzala m'Kacisi.

Yesaya 6

Yesaya 6:1-10