Yesaya 5:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo adzawabangulira tsiku limenelo ngati kukokoma kwa nyanja; ndipo wina ayang'ana padziko, taonani mdima ndi nsautso, kuyera kwadetsedwanso m'mitambo yace.

Yesaya 5

Yesaya 5:23-30