Yesaya 59:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace ciweruziro ciri patari ndi ife, ndi cilungamo sicitipeza; tiyang'anira kuunika, koma taona mdima; tiyang'anira kuyera, koma tiyenda m'usiku.

Yesaya 59

Yesaya 59:1-11