Yesaya 59:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Njira ya mtendere saidziwa, ndipo palibe ciweruziro m'mayendedwe mwao; akhotetsa njira zao; ali yense ayenda m'menemo sadziwa mtendere.

Yesaya 59

Yesaya 59:2-17