Yesaya 59:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mapazi ao athamangira koipa, ndipo iwo afulumira kukhetsa mwazi wosacimwa; maganizo ao ali maganizo oipa; bwinja ndi cipasuko ziri m'njira mwao.

Yesaya 59

Yesaya 59:1-11