Yesaya 59:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Palibe woturutsa mlandu molungama, ndipo palibe wonena zoona; iwo akhulupirira mwacabe, nanena zonama; iwo atenga kusayeruzika ndi kubala mphulupulu,

Yesaya 59

Yesaya 59:1-5