Yesaya 59:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwo afungatira mazira a mamba aswetse, naluka ukonde wa tandaude; iye amene adya mazira ace amafa, ndi coswanyikaco cisweka nicikhala songo.

Yesaya 59

Yesaya 59:1-9