Yesaya 59:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti manja anu adetsedwa ndi mwazi, ndi zala zanu ndi mphulupulu, milomo yanu yanena zonama, lilime lanu lilankhula moipa.

Yesaya 59

Yesaya 59:1-10