Yesaya 53:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaika manda ace pamodzi ndi oipa, ndi pamodzi ndi olemera mu imfa yace, ngakhale Iye sanacita ciwawa, ndipo m'kamwa mwace munalibe cinyengo.

Yesaya 53

Yesaya 53:1-12