Yesaya 53:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anacotsedwa ku cipsinjo ndi ciweruziro; ndipo ndani adzafotokoza nthawi ya moyo wace? pakuti walikhidwa kunja kuno; cifukwa ca kulakwa kwa anthu anga Iye anakhomedwa.

Yesaya 53

Yesaya 53:1-12