Yesaya 53:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iye anatsenderezedwa koma anadzicepetsa yekha osatsegula pakamwa pace; ngati nkhosa yotsogoleredwa kukaphedwa, ndi ngati mwana wa nkhosa amene ali du pamaso pa omsenga, motero sanatsegula pakamwa pace.

Yesaya 53

Yesaya 53:1-11