Yesaya 53:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma kunakomera Yehova kumtundudza; anammvetsa zowawa; moyo wace ukapereka nsembe yoparamula, Iye adzaona mbeu yace, adzatanimphitsa masiku ace; ndipo comkondweretsa Yehova cidzakula m'manja mwace.

Yesaya 53

Yesaya 53:8-12