Yesaya 48:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Imvani inu ici, banja la Yakobo, amene muchedwa ndi dzina la Israyeli, amene munaturuka m'madzi a Yuda amene mulumbira dzina la Yehova ndi kuchula dzina la Mulungu wa Israyeli, koma si m'zoona, pena m'cilungamo.

Yesaya 48

Yesaya 48:1-11