Yesaya 48:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti adziyesa okha a mudzi wopatulika, ndi kudzikhazikitsa iwo okha pa Mulungu wa Israyeli; dzina lace ndi Yehova wa makamu.

Yesaya 48

Yesaya 48:1-7