Yesaya 47:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zinthu zomwe unagwira nchito yace, zidzatero nawe; iwo amene anacita malonda ndi iwe ciyambire pa ubwana wako, adzayenda yense kunka kumalo kwace; sipadzakhala wopulumutsa iwe.

Yesaya 47

Yesaya 47:12-15