Yesaya 47:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taona, iwo adzakhala ngati ziputu, moto udzawatentha iwo; sadzadzipulumutsa okha ku mphamvu za malawi; motowo sudzakhala khala loothako, pena moto wakukhalako.

Yesaya 47

Yesaya 47:4-15