Yesaya 41:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwe udzawakupa, ndi mphepo idzawauluza; ndipo kabvumvulu adzawamwaza; ndipo iwe udzasangalala mwa Yehova, udzadzikuza mwa Woyera wa Israyeli,

Yesaya 41

Yesaya 41:11-24