Yesaya 41:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wosauka ndi wosowa afuna madzi, ndipo palibe, ndi lilume lao lilephera, cifukwa ca ludzu; Ine Yehova ndidzawayankha, Ine Mulungu wa Israyeli sindidzawasiya.

Yesaya 41

Yesaya 41:11-23