Yesaya 41:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taona, ndidzakuyesa iwe coombera tirigu catsopano cakuthwa cokhala ndi mano; iwe udzaomba mapiri ndi kuwapera asalale, ndi kusandutsa zitunda mungu.

Yesaya 41

Yesaya 41:13-17