Yesaya 39:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadza Yesaya mneneri kwa mfumu Hezekiya, nati kwa iye, Kodi anthu awa ananena bwanji, ndipo iwo acokera kuti, kudza kwa inu? Ndipo Hezekiya anati, Iwo acokera ku dziko lakutari, kudza kwa ine, kunena ku Babulo.

Yesaya 39

Yesaya 39:1-5