Yesaya 39:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anati, Kodi iwo anaona ciani m'nyumba mwanu? Ndipo Hezekiya anayankha, Zonse za m'nyumba mwanga iwo anaziona; palibe kanthu ka mwa cuma canga, kamene ine sindinawaonetse.

Yesaya 39

Yesaya 39:1-8