Yesaya 39:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Hezekiya anakondwera nao, nawaonetsa nyumba yace ya cuma, siliva, ndi golidi, ndi zonunkhira, ndi mafuta okometsetsa, ndi nyumba yonse ya zida zace, ndi zonse zopezedwa m'zosungira zace; munalibe kanthu m'nyumba mwace, kapena m'dziko lace lonse, kamene Hezekiya sanawaonetsa.

Yesaya 39

Yesaya 39:1-4