Yesaya 37:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

awa ndiwo mau amene Yehova wanena za iye, Namwali, mwana wamkazi wa Ziyoni, wakunyoza iwe ndi kuseka iwe ndi ciphwete; mwana wamkazi wa Yerusalemu wapukusa mutu wace pambuyo pako.

Yesaya 37

Yesaya 37:14-25