Yesaya 37:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndani amene, iwe wamtonza ndi kumlalatira? ndani amene iwe wakwezera mau ako ndi kutukulira maso ako kumwamba? ndiye Woyera wa Israyeli.

Yesaya 37

Yesaya 37:20-26