Yesaya 37:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yesaya, mwana wa Amozi, anatumiza kwa Hezekiya, ndi kuti, Atero Yehova, Mulungu wa Israyeli, Popeza wandipemphera za Sanakeribu mfumu ya Asuri,

Yesaya 37

Yesaya 37:13-25