Yesaya 25:11-12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

11. Ndipo iye adzatambasula manja ace pakati pamenepo, monga wosambira atambasula manja ace posambira; koma Iye adzagwetsa pansi kunyada kwace, pamodzi ndi kunyenga kwa manja ace.

12. Ndipo linga la pamsanje la macemba ako Iye waligwetsa, naligonetsa pansi, nalifikitsa padothi, ngakhale papfumbi.

Yesaya 25