Yesaya 24:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pompo mwezi udzanyazitsidwa, ndi dzuwa lidzakhala ndi manyazi, pakuti Yehova wa makamu adzalamulira caulemerero m'phiri la Ziyoni, ndi m'Yerusalemu, ndi pamaso pa akuru akuru ace.

Yesaya 24

Yesaya 24:14-23