Yesaya 24:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo adzasonkhanitsidwa pamodzi, monga ndende zimasonkhanitsidwa m'dzenje, ndi kutsekeredwa m'kaidi, ndipo atapita masiku ambiri adzawazonda.

Yesaya 24

Yesaya 24:16-23