Yesaya 26:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsiku limenelo adzayimba nyimbo imeneyi m'dziko la Yuda, Ife tiri ndi mudzi wolimba; Iye adzaikacipulumutso cikhale macemba ndi malinga.

Yesaya 26

Yesaya 26:1-4